Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu wosaugwira mtima ali ngati mzinda umene mpanda wake wagumulidwa, n’kuusiya wopanda mpanda.+ Amosi 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho, munthu wozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo chifukwa chakuti idzakhala nthawi yoopsa.+
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+
28 Munthu wosaugwira mtima ali ngati mzinda umene mpanda wake wagumulidwa, n’kuusiya wopanda mpanda.+
13 Choncho, munthu wozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo chifukwa chakuti idzakhala nthawi yoopsa.+