Mlaliki 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Usamapupulume kulankhula, ndipo mtima wako+ usamafulumire kulankhula pamaso pa Mulungu woona,+ chifukwa Mulungu woona ali kumwamba+ koma iwe uli padziko lapansi. N’chifukwa chake suyenera kulankhula zambiri.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
2 Usamapupulume kulankhula, ndipo mtima wako+ usamafulumire kulankhula pamaso pa Mulungu woona,+ chifukwa Mulungu woona ali kumwamba+ koma iwe uli padziko lapansi. N’chifukwa chake suyenera kulankhula zambiri.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+