Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zolinga za munthu wakhama zimam’pindulira,+ koma aliyense wopupuluma, ndithu adzasauka.+
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+