Yohane 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lilibe chifukwa chodana ndi inu, koma limadana ndi ine, chifukwa ndimachitira umboni kuti dzikoli ntchito zake ndi zoipa.+ 1 Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale, musadabwe kuti dziko limakudani.+
7 Dziko lilibe chifukwa chodana ndi inu, koma limadana ndi ine, chifukwa ndimachitira umboni kuti dzikoli ntchito zake ndi zoipa.+