Mateyu 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine. Yohane 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati dziko likudana nanu, mukudziwa kuti linadana ndi ine lisanadane ndi inu.+ 2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+
11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine.
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+