Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+ Luka 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma nzika zinzake zinadana naye+ ndipo m’mbuyo muno zinatumiza akazembe kuti apite akanene kuti, ‘Ife sitikufuna kuti munthu uyu akhale mfumu yathu.’+ Yohane 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo ndawapatsa mawu anu, koma dziko likudana nawo,+ chifukwa sali mbali ya dziko, monganso ine sindili mbali ya dziko.+ 1 Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale, musadabwe kuti dziko limakudani.+
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+
14 Koma nzika zinzake zinadana naye+ ndipo m’mbuyo muno zinatumiza akazembe kuti apite akanene kuti, ‘Ife sitikufuna kuti munthu uyu akhale mfumu yathu.’+
14 Iwo ndawapatsa mawu anu, koma dziko likudana nawo,+ chifukwa sali mbali ya dziko, monganso ine sindili mbali ya dziko.+