Yohane 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anawauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano, ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera m’dziko lino,+ ine si wochokera m’dziko lino.+ Yohane 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+ Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+
23 Iye anawauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano, ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera m’dziko lino,+ ine si wochokera m’dziko lino.+
19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+
4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+