Miyambo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nawa mawu a Aguri mwana wa Yake, mwamuna wamphamvu. Mawuwa anali uthenga wamphamvu+ womwe iye analankhula ndi Itiyeli, ndi Itiyeli ndiponso Ukali, kuti: 2 Timoteyo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+
30 Nawa mawu a Aguri mwana wa Yake, mwamuna wamphamvu. Mawuwa anali uthenga wamphamvu+ womwe iye analankhula ndi Itiyeli, ndi Itiyeli ndiponso Ukali, kuti:
16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+