Salimo 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzatchera khutu kuti ndimvetsere mwambi.+Poimba zeze ndidzamasulira mawu anga ophiphiritsa.+