Miyambo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 kuti azitha kumvetsa mwambi ndi mawu ozunguza mutu,+ mawu a anthu anzeru+ ndi mikuluwiko yawo.+