Miyambo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga, zimenezi zisachoke pamaso pako.+ Usunge nzeru zopindulitsa ndiponso kuganiza bwino,+