Miyambo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yothandiza kuti munthu wosadziwa akhale wochenjera,+kuti wachinyamata akhale wodziwa zinthu+ ndiponso kuti azitha kuganiza bwino.+ Miyambo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti uteteze kuganiza bwino,+ ndiponso kuti milomo yako iteteze kudziwa zinthu.+
4 Yothandiza kuti munthu wosadziwa akhale wochenjera,+kuti wachinyamata akhale wodziwa zinthu+ ndiponso kuti azitha kuganiza bwino.+