Yoswa 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atamva choncho, paokha anachitapo kanthu mwanzeru.+ Ananyamula chakudya m’matumba akutha n’kukweza pa abulu awo. Ananyamulanso vinyo m’matumba achikopa akutha, omangamanga mong’ambika.+ 1 Samueli 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chonde pitani, mukayesetsebe kufufuza kwa aliyense amene anamuonayo, ndipo mukaone kumene iye amafika, pakuti ndauzidwa kuti ndi wochenjera kwambiri.+ Miyambo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense wopusa amanyoza malangizo* a bambo ake,+ koma munthu aliyense womvera chidzudzulo ndi wochenjera.+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
4 Atamva choncho, paokha anachitapo kanthu mwanzeru.+ Ananyamula chakudya m’matumba akutha n’kukweza pa abulu awo. Ananyamulanso vinyo m’matumba achikopa akutha, omangamanga mong’ambika.+
22 Chonde pitani, mukayesetsebe kufufuza kwa aliyense amene anamuonayo, ndipo mukaone kumene iye amafika, pakuti ndauzidwa kuti ndi wochenjera kwambiri.+
5 Aliyense wopusa amanyoza malangizo* a bambo ake,+ koma munthu aliyense womvera chidzudzulo ndi wochenjera.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+