Miyambo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuganiza bwino kudzakuyang’anira,+ ndipo kuzindikira kudzakuteteza,+ Miyambo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga, zimenezi zisachoke pamaso pako.+ Usunge nzeru zopindulitsa ndiponso kuganiza bwino,+ Miyambo 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine nzeru, ndimakhala pamodzi ndi kuchenjera,+ ndimadziwa zinthu, ndiponso ndimatha kuganiza bwino.+ Miyambo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu amene amakwiya msanga amachita zinthu zopusa,+ koma munthu wotha kuganiza bwino amadedwa.+
12 “Ine nzeru, ndimakhala pamodzi ndi kuchenjera,+ ndimadziwa zinthu, ndiponso ndimatha kuganiza bwino.+