Mlaliki 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati nkhwangwa yabuntha ndipo munthu sanainole,+ adzawononga mphamvu zake pachabe. Choncho kugwiritsa ntchito bwino nzeru kumapindulitsa.+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
10 Ngati nkhwangwa yabuntha ndipo munthu sanainole,+ adzawononga mphamvu zake pachabe. Choncho kugwiritsa ntchito bwino nzeru kumapindulitsa.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+