Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 31:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo ndidzam’patsa mzimu wa Mulungu kuti akhale wanzeru, wozindikira, wodziwa zinthu, ndi kuti akhale mmisiri waluso pa ntchito ina iliyonse.+

  • 2 Mbiri 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ameneyu ndi mwana wa mayi winawake wa fuko la Dani, koma bambo ake anali a ku Turo. Iye ndi wodziwa ntchito zagolide, zasiliva, zamkuwa,+ zachitsulo, zamiyala,+ ndi zamatabwa. Amadziwanso ntchito za ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira+ ndi utoto wabuluu,+ komanso ntchito za nsalu+ zabwino kwambiri ndi zofiira.+ Iye amadziwanso ntchito zamtundu uliwonse zojambula ndi kulemba mochita kugoba.+ Amadziwanso ntchito zokonza zipangizo zamtundu uliwonse+ zimene angapatsidwe kuti achite pamodzi ndi anthu anu aluso ndi anthu aluso a mbuye wanga Davide bambo anu.

  • Mlaliki 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena