1 Samueli 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Aisiraeli onse akafuna kunola pulawo, khasu, nkhwangwa kapena chikwakwa, aliyense wa iwo anali kupita kwa Afilisiti kuti amunolere.+
20 Choncho Aisiraeli onse akafuna kunola pulawo, khasu, nkhwangwa kapena chikwakwa, aliyense wa iwo anali kupita kwa Afilisiti kuti amunolere.+