Miyambo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu amene amasonyeza mkwiyo wake tsiku lomwelo ndi wopusa,+ koma wochenjera akachitiridwa chipongwe, amangozinyalanyaza.+ Miyambo 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+
16 Munthu amene amasonyeza mkwiyo wake tsiku lomwelo ndi wopusa,+ koma wochenjera akachitiridwa chipongwe, amangozinyalanyaza.+
32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+