Miyambo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wopusa amatulutsa mkwiyo* wake wonse, koma wanzeru amakhala wodekha mpaka pamapeto.+