Miyambo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uipewe,+ uilambalale.+ Upatukepo, n’kupitirira.+ Miyambo 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kodi munthu anganyamule makala a moto pachifuwa pake, zovala zake osapsa?+ Miyambo 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wakhala pampando pakhomo la nyumba yake, pachitunda cha m’mudzimo,+