Miyambo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amapezeka panja, m’mabwalo a mzinda,+ ndiponso amakhala akudikirira anthu pafupi ndi mphambano iliyonse.+ Miyambo 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithudi iye mofanana ndi wachifwamba,+ amabisalira anthu panjira, ndipo amachulukitsa amuna achinyengo.+
12 Amapezeka panja, m’mabwalo a mzinda,+ ndiponso amakhala akudikirira anthu pafupi ndi mphambano iliyonse.+
28 Ndithudi iye mofanana ndi wachifwamba,+ amabisalira anthu panjira, ndipo amachulukitsa amuna achinyengo.+