Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ineyo ndikhala chikole cha moyo wa mnyamatayu.+ Chilangocho chikabwere pa ine.+ Ndikadzalephera kubwera naye ndi kum’pereka kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu moyo wanga wonse.

  • Miyambo 17:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+

  • Miyambo 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Usakhale pakati pa anthu ogwirana chanza,+ pakati pa anthu amene amakhala chikole cha ngongole za anthu ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena