Miyambo 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Monga momwe chimakhalira chipini* chagolide pamphuno ya nkhumba, ndi mmenenso amakhalira mkazi wokongola koma wosaganiza bwino.+ Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+ Yakobo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+
22 Monga momwe chimakhalira chipini* chagolide pamphuno ya nkhumba, ndi mmenenso amakhalira mkazi wokongola koma wosaganiza bwino.+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+