Yesaya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wati: “Ana aakazi a Ziyoni ndi odzikuza. Iwo amayenda atasolola makosi awo ndiponso amakopa amuna ndi maso awo. Amayenda modzigomera, ndipo akamayenda mapazi awo amachita phokoso chifukwa cha zokongoletsera zimene amavala m’mapazi.+
16 Yehova wati: “Ana aakazi a Ziyoni ndi odzikuza. Iwo amayenda atasolola makosi awo ndiponso amakopa amuna ndi maso awo. Amayenda modzigomera, ndipo akamayenda mapazi awo amachita phokoso chifukwa cha zokongoletsera zimene amavala m’mapazi.+