Miyambo 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mkazi wopusa amakhala wolongolola.+ Iye ndi woperewera nzeru ndipo sadziwa chilichonse.+