Miyambo 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 wolongolola ndiponso wamakani.*+ Mapazi ake sakhala m’nyumba mwake.+ Miyambo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+
9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+