Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Timoteyo 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Komanso pa nthawi yomweyo, amayamba chizolowezi chomangokhala osachita kanthu, n’kumangoyendayenda m’makomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakhalanso amiseche ndi olowerera nkhani za eni,+ n’kumalankhula zimene sayenera kulankhula.

  • Tito 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena