Genesis 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+ 1 Akorinto 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 akazi akhale chete+ m’mipingo, pakuti sikololeka kuti iwo azilankhula, koma akhale ogonjera,+ monga Chilamulo+ chimanenera.
16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+
34 akazi akhale chete+ m’mipingo, pakuti sikololeka kuti iwo azilankhula, koma akhale ogonjera,+ monga Chilamulo+ chimanenera.