1 Timoteyo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Onse amene ali m’goli laukapolo, aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwapatsa ulemu wawo wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndi chiphunzitsocho asazinenere zoipa.+ 2 Timoteyo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chita chilichonse chotheka kuti usonyeze kuti ndiwe wovomerezeka+ pamaso pa Mulungu, wantchito+ wopanda chifukwa chochitira manyazi+ ndi ntchito imene wagwira, ndiponso wophunzitsa ndi kufotokoza bwino mawu a choonadi.+
6 Onse amene ali m’goli laukapolo, aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwapatsa ulemu wawo wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndi chiphunzitsocho asazinenere zoipa.+
15 Chita chilichonse chotheka kuti usonyeze kuti ndiwe wovomerezeka+ pamaso pa Mulungu, wantchito+ wopanda chifukwa chochitira manyazi+ ndi ntchito imene wagwira, ndiponso wophunzitsa ndi kufotokoza bwino mawu a choonadi.+