Aroma 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera. Tito 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+ 1 Petulo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha Ambuye, gonjerani+ dongosolo lililonse lopangidwa ndi anthu:+ kaya mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,
24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera.
5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+
13 Chifukwa cha Ambuye, gonjerani+ dongosolo lililonse lopangidwa ndi anthu:+ kaya mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,