2 Atesalonika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti tikumva kuti ena akuyenda mosalongosoka+ pakati panu, sakugwira ntchito n’komwe, koma akulowerera nkhani zimene sizikuwakhudza.+ 1 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+ 1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+
11 Pakuti tikumva kuti ena akuyenda mosalongosoka+ pakati panu, sakugwira ntchito n’komwe, koma akulowerera nkhani zimene sizikuwakhudza.+
11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+
15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+