Miyambo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti usapereke ulemu wako kwa anthu ena+ kapena kupereka zaka zako ku zinthu zankhanza.+ Miyambo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 komanso kuti usadzabuule m’tsogolo+ mnofu ndi thupi lako zikadzafika ku mapeto kwake.+