Miyambo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 komanso ukaitana kumvetsa zinthu+ ndi kufuulira kuzindikira,+ Miyambo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuganiza bwino kudzakuyang’anira,+ ndipo kuzindikira kudzakuteteza,+