Maliko 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 amene panopa sadzapeza zochuluka kuwirikiza maulendo 100+ m’nthawi* ino. Iye adzapeza nyumba, abale, alongo, amayi, ana ndi minda, limodzi ndi mazunzo,+ ndipo m’nthawi imene ikubwerayo, adzapeza moyo wosatha.
30 amene panopa sadzapeza zochuluka kuwirikiza maulendo 100+ m’nthawi* ino. Iye adzapeza nyumba, abale, alongo, amayi, ana ndi minda, limodzi ndi mazunzo,+ ndipo m’nthawi imene ikubwerayo, adzapeza moyo wosatha.