Genesis 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uziti ukalima, nthaka sizikubalira mokwanira.+ Udzakhala moyo woyendayenda ndi wothawathawa padziko lapansi.”+ Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+
12 Uziti ukalima, nthaka sizikubalira mokwanira.+ Udzakhala moyo woyendayenda ndi wothawathawa padziko lapansi.”+
7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+