Salimo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amadziwa njira za olungama,+Koma oipa adzatheratu pamodzi ndi njira zawo.+ Salimo 146:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+ Mateyu 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Lowani pachipata chopapatiza.+ Pakuti msewu waukulu ndi wotakasuka ukupita kuchiwonongeko, ndipo anthu ambiri akuyenda mmenemo.
9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+
13 “Lowani pachipata chopapatiza.+ Pakuti msewu waukulu ndi wotakasuka ukupita kuchiwonongeko, ndipo anthu ambiri akuyenda mmenemo.