Miyambo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wanga, ochimwa akayesa kukunyengerera usavomere.+ 2 Petulo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho inu okondedwa, popeza mukudziwiratu zimenezi,+ chenjerani kuti musasochere pokopeka ndi zolakwa za anthu ophwanya malamulowo, kuopera kuti mungalephere kukhala olimba ndipo mungagwe.+
17 Choncho inu okondedwa, popeza mukudziwiratu zimenezi,+ chenjerani kuti musasochere pokopeka ndi zolakwa za anthu ophwanya malamulowo, kuopera kuti mungalephere kukhala olimba ndipo mungagwe.+