Salimo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+ Miyambo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amatsinzinira ena ndi diso lake,+ amapanga zizindikiro ndi phazi lake, ndiponso amapanga zizindikiro ndi zala zake.+
19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+
13 Amatsinzinira ena ndi diso lake,+ amapanga zizindikiro ndi phazi lake, ndiponso amapanga zizindikiro ndi zala zake.+