1 Samueli 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atatero, Davide analandira zimene Abigayeli anamubweretsera ndiyeno anamuuza kuti: “Pita kunyumba kwako mwamtendere.+ Taona, ndamvera mawu ako kuti ndichite zinthu mokuganizira.”+
35 Atatero, Davide analandira zimene Abigayeli anamubweretsera ndiyeno anamuuza kuti: “Pita kunyumba kwako mwamtendere.+ Taona, ndamvera mawu ako kuti ndichite zinthu mokuganizira.”+