Miyambo 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale utasinja chitsiru mumtondo ndi musi limodzi ndi mbewu, uchitsiru wake sungachichokere.+