Miyambo 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakamwa pa wolungama pamabala zipatso za nzeru,+ koma lilime lonena zopotoka lidzadulidwa.+ Miyambo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Milomo ya munthu wopusa imalowa mu mkangano,+ ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+ Mlaliki 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+ Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+
12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+
8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+