1 Mafumu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’makalatamo analembamo kuti:+ “Uzani anthu kuti asale kudya, ndipo muike Naboti patsogolo pa anthu onse. Yesaya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsoka kwa anthu amene amanena kuti woipa ndi wolungama chifukwa cholandira chiphuphu,+ ndiponso kwa amene amanena kuti wolungama ndi wolakwa.+
9 M’makalatamo analembamo kuti:+ “Uzani anthu kuti asale kudya, ndipo muike Naboti patsogolo pa anthu onse.
23 Tsoka kwa anthu amene amanena kuti woipa ndi wolungama chifukwa cholandira chiphuphu,+ ndiponso kwa amene amanena kuti wolungama ndi wolakwa.+