Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Yobu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ungazindikire zinthu zozama za Mulungu,+Kapena kodi ungadziwe mapeto a kukula kwa Wamphamvuyonse?
7 Kodi ungazindikire zinthu zozama za Mulungu,+Kapena kodi ungadziwe mapeto a kukula kwa Wamphamvuyonse?