Hoseya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Alendo alanda mphamvu zake,+ ndipo iye sakudziwa zimenezi.+ Mutu wake wonse wangoti mbuu ndi imvi, koma iye sakudziwa zimenezi.
9 Alendo alanda mphamvu zake,+ ndipo iye sakudziwa zimenezi.+ Mutu wake wonse wangoti mbuu ndi imvi, koma iye sakudziwa zimenezi.