2 Mafumu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho mkwiyo wa Yehova+ unawayakira Aisiraeli, moti nthawi zonse ankawapereka m’manja mwa Hazaeli+ mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa Beni-hadadi+ mwana wa Hazaeli. 2 Mafumu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Puli+ mfumu ya Asuri+ inabwera m’dzikomo. Choncho Menahemu anapatsa+ Puli matalente* 1,000 a siliva,+ kuti amuthandize kulimbitsa ufumu umene unali m’manja mwake.+
3 Choncho mkwiyo wa Yehova+ unawayakira Aisiraeli, moti nthawi zonse ankawapereka m’manja mwa Hazaeli+ mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa Beni-hadadi+ mwana wa Hazaeli.
19 Tsopano Puli+ mfumu ya Asuri+ inabwera m’dzikomo. Choncho Menahemu anapatsa+ Puli matalente* 1,000 a siliva,+ kuti amuthandize kulimbitsa ufumu umene unali m’manja mwake.+