Numeri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+ Yakobo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumalakalaka, koma simukhala nazo. Mumapha anthu+ ndiponso mumasirira mwansanje,+ koma simupeza kanthu. Mumakangana+ ndiponso mumachita nkhondo. Simukhala ndi kanthu chifukwa simupempha.
4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+
2 Mumalakalaka, koma simukhala nazo. Mumapha anthu+ ndiponso mumasirira mwansanje,+ koma simupeza kanthu. Mumakangana+ ndiponso mumachita nkhondo. Simukhala ndi kanthu chifukwa simupempha.