Salimo 119:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Zili bwino kuti ndasautsika,+Kuti ndiphunzire malamulo anu.+ Luka 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Inu amene mukumva njala+ tsopano ndinu odala, chifukwa mudzakhuta.+ “Inu amene mukulira tsopano ndinu odala, chifukwa mudzaseka.+
21 “Inu amene mukumva njala+ tsopano ndinu odala, chifukwa mudzakhuta.+ “Inu amene mukulira tsopano ndinu odala, chifukwa mudzaseka.+