1 Samueli 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Samueli anati: “M’bweretseni kuno Agagi mfumu ya Amaleki.” Atatero, Agagi anapita kwa Samueli mwamantha ndi mokayikira.* Mumtima mwake Agagi anayamba kunena kuti: “Ndithudi, ululu wa imfa wachoka.” Salimo 55:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga ukundipweteka kwambiri.+Ndipo ndikuopa imfa.+
32 Kenako Samueli anati: “M’bweretseni kuno Agagi mfumu ya Amaleki.” Atatero, Agagi anapita kwa Samueli mwamantha ndi mokayikira.* Mumtima mwake Agagi anayamba kunena kuti: “Ndithudi, ululu wa imfa wachoka.”