Genesis 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe wotimasulira malotowo.” Pamenepo Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu sindiye amamasulira?+ Tandifotokozerani malotowo.” 2 Petulo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choyamba, mukudziwa kuti ulosi wa m’Malemba suchokera m’maganizo a munthu.+
8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe wotimasulira malotowo.” Pamenepo Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu sindiye amamasulira?+ Tandifotokozerani malotowo.”