Luka 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komatu palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndi chinsinsi chimene sichidzadziwika.+